Yeremiya 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wandiuza kuti, ‘Upange zomangira ndiponso magoli,+ ndipo uzivale m’khosi mwako.+ Yeremiya 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hananiya atamva zimenezo anatenga goli limene linali m’khosi mwa mneneri Yeremiya ndipo analithyola.+
10 Hananiya atamva zimenezo anatenga goli limene linali m’khosi mwa mneneri Yeremiya ndipo analithyola.+