Yeremiya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova. Ezekieli 36:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu mudzakhala m’dziko limene ndinapatsa makolo anu.+ Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+ Aheberi 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.
31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
28 Inu mudzakhala m’dziko limene ndinapatsa makolo anu.+ Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+
10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.