Yesaya 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malo ouma chifukwa cha kutentha adzakhala dambo la madzi, ndipo malo aludzu adzakhala malo a akasupe amadzi.+ Kumalo okhala mimbulu,+ malo ake ousako, kudzakhala udzu wobiriwira, mabango ndi gumbwa.+ Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+
7 Malo ouma chifukwa cha kutentha adzakhala dambo la madzi, ndipo malo aludzu adzakhala malo a akasupe amadzi.+ Kumalo okhala mimbulu,+ malo ake ousako, kudzakhala udzu wobiriwira, mabango ndi gumbwa.+
10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+