Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+

  • Zekariya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova wa makamu adzatchinjiriza anthu ake. Adani awo adzawalasa ndi miyala yoponya ndi gulaye* koma iwo adzagonjetsa adaniwo.+ Iwo adzasangalala ndipo adzafuula ngati amwa vinyo.+ Adzadzazidwa ngati mbale zolowa ndiponso ngati mmene magazi amadzazira m’makona a guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena