Levitiko 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo. Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+
41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo.
6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+