Ezekieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+ Ezekieli 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+
26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+