Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 54:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+

  • Yohane 6:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+

  • 1 Atesalonika 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma za kukonda abale,+ n’zosafunika kuti tizichita kukulemberani pakuti inu nomwe, Mulungu amakuphunzitsani+ kukondana.+

  • 1 Yohane 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Inuyo, Mulungu anakudzozani ndi mzimu+ ndipo mzimu umenewo udakali mwa inu. Chotero simukufunikira wina aliyense kuti azikuphunzitsani,+ koma popeza kuti munadzozedwadi moona+ osati monama, chifukwa cha kudzozedwako, mukuphunzitsidwa zinthu zonse.+ Monga mmene mwaphunzitsidwira, pitirizani kukhala ogwirizana+ naye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena