2 Mafumu 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+ 2 Mbiri 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anam’gwira n’kutuluka naye. Atangofika pakhomo la kunyumba ya mfumu lolowera mahatchi, anam’phera pomwepo.+ Nehemiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ansembe anakonza mpandawo kuyambira kumtunda kwa Chipata cha Hatchi,+ ndipo aliyense anali kukonza patsogolo pa nyumba yake.
16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+
15 Choncho anam’gwira n’kutuluka naye. Atangofika pakhomo la kunyumba ya mfumu lolowera mahatchi, anam’phera pomwepo.+
28 Ansembe anakonza mpandawo kuyambira kumtunda kwa Chipata cha Hatchi,+ ndipo aliyense anali kukonza patsogolo pa nyumba yake.