Levitiko 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera m’Chaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene udzakhala ukukololapo.+
15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera m’Chaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene udzakhala ukukololapo.+