Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+

  • 2 Samueli 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndi mtundu uti padziko lapansi umene ungafanane ndi mtundu wa anthu anu Aisiraeli,+ amene inu Mulungu munawawombola monga anthu anu+ ndi kudzipangira dzina,+ amene munawachitira zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha?+ Munapitikitsa mitundu ina ndi milungu yawo, chifukwa cha anthu anu amene munawawombola+ nokha kuchokera ku Iguputo.

  • Yesaya 63:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ali kuti amene anachititsa mkono wake wokongola+ kupita kudzanja lamanja la Mose, amene anagawanitsa madzi pamaso pawo+ kuti adzipangire dzina lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+

  • Danieli 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Tsopano inu Yehova Mulungu wathu, amene munatulutsa anthu anu m’dziko la Iguputo ndi dzanja lamphamvu,+ amenenso munadzipangira dzina kufikira lero,+ ife tachimwa,+ tachita zinthu zoipa.

  • Aroma 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena