Salimo 105:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+ Salimo 106:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo pang’onopang’ono nyanjayo inauma.+Pamenepo anawayendetsa kudutsa pakati pa madzi akuya ngati akuwayendetsa m’chipululu.+
9 Choncho anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo pang’onopang’ono nyanjayo inauma.+Pamenepo anawayendetsa kudutsa pakati pa madzi akuya ngati akuwayendetsa m’chipululu.+