Nehemiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo munawachulukitsira ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Mutatero munawalowetsa m’dziko+ limene munalonjeza makolo awo+ kuti akalowe ndi kulitenga. Salimo 105:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+
23 Ndipo munawachulukitsira ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Mutatero munawalowetsa m’dziko+ limene munalonjeza makolo awo+ kuti akalowe ndi kulitenga.
44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+