Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Danieli 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sitinamvere mawu anu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kuyenda motsatira malamulo anu amene munatiikira kudzera mwa atumiki anu, aneneri.+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
10 Sitinamvere mawu anu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kuyenda motsatira malamulo anu amene munatiikira kudzera mwa atumiki anu, aneneri.+