Numeri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+ Numeri 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inu Yehova, Mulungu wa miyoyo ya zamoyo+ zamitundu yonse,+ sankhani munthu woti aziyang’anira khamuli.+ Luka 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse adzaona njira ya Mulungu yopulumutsira.’”+ Aroma 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+
22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+
16 “Inu Yehova, Mulungu wa miyoyo ya zamoyo+ zamitundu yonse,+ sankhani munthu woti aziyang’anira khamuli.+
29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+