Deuteronomo 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+ Ezekieli 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzakhala m’dzikolo popanda chowaopseza,+ adzamanga nyumba+ ndi kulima minda ya mpesa.+ Iwo adzakhala mwabata+ ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene akuwatonza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”
28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+
26 Adzakhala m’dzikolo popanda chowaopseza,+ adzamanga nyumba+ ndi kulima minda ya mpesa.+ Iwo adzakhala mwabata+ ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene akuwatonza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”