Yeremiya 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mitunduyo ndi iyi: Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda pamodzi ndi mafumu ake ndi akalonga ake. Ndinawamwetsa kuti mizinda yawo ikhale bwinja, chinthu chodabwitsa+ chimene anthu azidzachiimbira mluzu, ndiponso kuti ikhale yotembereredwa. Zimenezi zatsala pang’ono kuchitika.+ Danieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+
18 Mitunduyo ndi iyi: Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda pamodzi ndi mafumu ake ndi akalonga ake. Ndinawamwetsa kuti mizinda yawo ikhale bwinja, chinthu chodabwitsa+ chimene anthu azidzachiimbira mluzu, ndiponso kuti ikhale yotembereredwa. Zimenezi zatsala pang’ono kuchitika.+
6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+