2 Mbiri 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Hezekiya anawauza kuti akonze zipinda zodyera+ m’nyumba ya Yehova, ndipo iwo anakonzadi.