Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, sunga lamulo la bambo ako,+ ndipo usasiye malangizo a mayi ako.+