Yeremiya 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mneneri Yeremiya analankhula ndi Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Barukiyo anali kulemba mawu a Yeremiya m’buku.+ Chimenechi chinali chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiyayo anati:
45 Mneneri Yeremiya analankhula ndi Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Barukiyo anali kulemba mawu a Yeremiya m’buku.+ Chimenechi chinali chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiyayo anati: