Yeremiya 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyo, magulu ankhondo a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu.+ Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera m’nyumba imene inali m’Bwalo la Alonda.+ Bwalo limeneli linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda.
2 Pa nthawi imeneyo, magulu ankhondo a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu.+ Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera m’nyumba imene inali m’Bwalo la Alonda.+ Bwalo limeneli linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda.