Yeremiya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova. Yeremiya 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pazipata izi.+
2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova.
2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pazipata izi.+