Yeremiya 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mikaya mwana wa Gemariya, mwana wa Safani,+ anamva mawu onse a Yehova amene anali mumpukutumo.