Amosi 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”
15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”