Yesaya 47:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwotu akhala ngati mapesi.+ Moto udzawatentha ndithu.+ Sadzapulumutsa moyo wawo+ ku mphamvu ya moto walawilawi.+ Sudzakhala moto wamakala woti anthu n’kumawotha. Sudzakhala moto wounikira woti anthu n’kuuyandikira.
14 Iwotu akhala ngati mapesi.+ Moto udzawatentha ndithu.+ Sadzapulumutsa moyo wawo+ ku mphamvu ya moto walawilawi.+ Sudzakhala moto wamakala woti anthu n’kumawotha. Sudzakhala moto wounikira woti anthu n’kuuyandikira.