Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+ Amosi 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+
10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+
10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+