Salimo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musandipereke kwa adani anga.+Pakuti mboni zonama zandiukira,+Chimodzimodzinso munthu wachiwawa.+ Salimo 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mboni zachiwawa zimaimirira.+Zimandifunsa zinthu zimene sindikudziwa.+