1 Samueli 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davideyo anawonjezera kuti: “N’chifukwa chiyani inu mbuyanga mukuthamangitsa ine mtumiki wanu?+ Ndachita chiyani ine, ndipo ndalakwa chiyani?+
18 Davideyo anawonjezera kuti: “N’chifukwa chiyani inu mbuyanga mukuthamangitsa ine mtumiki wanu?+ Ndachita chiyani ine, ndipo ndalakwa chiyani?+