Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+
9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+