Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+ Miyambo 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wachiwawa amakopa mnzake,+ ndipo amam’chititsa kuti ayende m’njira yoipa.+
9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+