Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kenako Farao Neko+ anamanga+ Yehoahazi ku Ribila+ m’dziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Ndiyeno Farao Neko analamula+ dzikolo kuti lim’patse matalente 100 a siliva+ ndi talente imodzi ya golide.+

  • 2 Mafumu 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Akasidiwo anagwira mfumuyo+ n’kupita nayo ku Ribila+ kwa mfumu ya Babulo, kuti akaiuze chigamulo chake.

  • 2 Mafumu 25:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+

  • Yeremiya 52:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa n’kupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena