Deuteronomo 28:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo udzasokonezeka mutu chifukwa cha zimene maso ako adzaona.+ Yesaya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa, iwo akuona.+ Katundu wa m’nyumba zawo adzalandidwa, ndipo akazi awo adzagwiriridwa.+
16 Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa, iwo akuona.+ Katundu wa m’nyumba zawo adzalandidwa, ndipo akazi awo adzagwiriridwa.+