Deuteronomo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+ 1 Mafumu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake, anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira. N’chifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+
9 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake, anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira. N’chifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+