-
Yeremiya 41:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Isimaeli anaphanso Ayuda onse amene anali ndi Gedaliya ku Mizipa pamodzi ndi Akasidi, amuna ankhondo, amene anawapeza kumeneko.
-