2 Samueli 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!”
17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anakantha Mfilisitiyo ndi kumupha. Pamenepo asilikali a Davide analumbira kwa iye kuti: “Simudzapitanso ndi ife kunkhondo,+ chifukwa mungazimitse+ nyale+ ya Isiraeli!”