2 Samueli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mwamuna wake anali kumutsatira. Iye anali kumutsatira pambuyo akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Pamenepo iye anabwerera.
16 Koma mwamuna wake anali kumutsatira. Iye anali kumutsatira pambuyo akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Pamenepo iye anabwerera.