2 Samueli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nayenso Yowabu+ mwana wa Zeruya+ ndi atumiki a Davide, anapita kudziwe la Gibeoni ndipo magulu awiriwo anakumana kumeneko. Gulu la Yowabu linangokhala pansi kumbali ina ya dziwe ndipo gulu linalo linakhalanso kumbali inayo.
13 Nayenso Yowabu+ mwana wa Zeruya+ ndi atumiki a Davide, anapita kudziwe la Gibeoni ndipo magulu awiriwo anakumana kumeneko. Gulu la Yowabu linangokhala pansi kumbali ina ya dziwe ndipo gulu linalo linakhalanso kumbali inayo.