Genesis 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+ Oweruza 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno mu Betelehemu+ wa ku Yuda munali mnyamata wina, wa m’banja la Yuda, ndipo anali Mlevi.+ Iye anakhala kumeneko kwa kanthawi. 1 Mbiri 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Salima bambo wa Betelehemu,+ ndi Harefi bambo wa Beti-gaderi.
19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+
7 Ndiyeno mu Betelehemu+ wa ku Yuda munali mnyamata wina, wa m’banja la Yuda, ndipo anali Mlevi.+ Iye anakhala kumeneko kwa kanthawi.