1 Mafumu 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+
14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+