Ekisodo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+ Deuteronomo 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’
8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+
27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’