Numeri 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinali kudya ku Iguputo,+ nkhaka, mavwende, adyo komanso anyezi wamitundumitundu!
5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinali kudya ku Iguputo,+ nkhaka, mavwende, adyo komanso anyezi wamitundumitundu!