Yeremiya 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+ Yeremiya 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano dziwani kuti, ndithu mudzafa ndi lupanga,+ njala yaikulu ndi mliri m’dziko limene mukulakalaka kukalowamo kuti mukakhale monga alendo kumeneko.”+
10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+
22 Tsopano dziwani kuti, ndithu mudzafa ndi lupanga,+ njala yaikulu ndi mliri m’dziko limene mukulakalaka kukalowamo kuti mukakhale monga alendo kumeneko.”+