Yesaya 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti akalonga ake afika ku Zowani,+ ndipo nthumwi zake zafika mpaka ku Hanesi. Yeremiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale anthu a ku Nofi+ ndi ku Tahapanesi+ anawononga dziko lako.*+ Yeremiya 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti: Ezekieli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mumzinda wa Tahapanesi+ mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amazinyadira zidzathetsedwa.+ Iye adzakutidwa ndi mitambo+ ndipo anthu a m’mizinda yake yozungulira adzatengedwa kupita ku ukapolo.+
44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:
18 Mumzinda wa Tahapanesi+ mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amazinyadira zidzathetsedwa.+ Iye adzakutidwa ndi mitambo+ ndipo anthu a m’mizinda yake yozungulira adzatengedwa kupita ku ukapolo.+