Yesaya 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+
2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+