Salimo 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+ Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+