1 Mafumu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ayuda anapitiriza kuchita zoipa m’maso mwa Yehova,+ moti anamuchititsa+ nsanje kuposa mmene makolo awo anamuchititsira nsanje ndi machimo awo onse amene makolowo anachita.+
22 Ayuda anapitiriza kuchita zoipa m’maso mwa Yehova,+ moti anamuchititsa+ nsanje kuposa mmene makolo awo anamuchititsira nsanje ndi machimo awo onse amene makolowo anachita.+