Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Abiyamu anapitiriza kuyenda m’machimo onse amene bambo ake anachita. Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+

  • 2 Mbiri 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ m’mapiri a ku Yuda kuti achititse anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ ndiponso kuti asocheretse Yuda.+

  • 2 Mbiri 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma pobwerera kuchokera kokapha Aedomu, Amaziya anatenga milungu+ ya ana a Seiri n’kukaiimika kuti ikhale milungu yake.+ Kenako anayamba kuigwadira+ ndi kuifukizira nsembe yautsi.+

  • 2 Mbiri 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho iye anamanganso malo okwezeka+ amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe+ a Abaala+ n’kumanga mizati yopatulika,+ ndipo anayamba kugwadira+ khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ n’kumazitumikira.+

  • Yeremiya 44:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ife tichita zonse zimene tanena.+ Tipereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa+ kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Tichita zimenezi monga mmene ife,+ makolo athu,+ mafumu athu+ ndi akalonga athu anachitira m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu pamene tinali kudya mkate ndi kukhuta ndipo zinthu zinali kutiyendera bwino, moti sitinaone tsoka lililonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena