Hoseya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+ Amosi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+
2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+
7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+