Ezekieli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano mapeto akufikira,+ ndipo ndikutumizira mkwiyo wanga. Ndikuweruza mogwirizana ndi njira zako+ ndipo ndikubwezera chifukwa cha zonyansa zako zonse.
3 Tsopano mapeto akufikira,+ ndipo ndikutumizira mkwiyo wanga. Ndikuweruza mogwirizana ndi njira zako+ ndipo ndikubwezera chifukwa cha zonyansa zako zonse.