1 Samueli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000.
5 Anali atavala chisoti chamkuwa kumutu kwake ndi chovala chamamba achitsulo. Mkuwa wa chovala chamamba chimenecho+ unali wolemera masekeli* 5,000.