2 Mafumu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yomweyo anthuwo ananyamuka n’kuyamba kuthawa kukungoyamba kumene kuda.+ Anasiya mahema awo, mahatchi awo,+ ndi abulu awo. Msasawo anausiya mmene unalili n’kuthawa kuti apulumutse miyoyo yawo.+
7 Nthawi yomweyo anthuwo ananyamuka n’kuyamba kuthawa kukungoyamba kumene kuda.+ Anasiya mahema awo, mahatchi awo,+ ndi abulu awo. Msasawo anausiya mmene unalili n’kuthawa kuti apulumutse miyoyo yawo.+